-
Yobu 7:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ngati ndachimwa, kodi zimakukhudzani bwanji, Inu amene mumayangʼanitsitsa anthu?+
Nʼchifukwa chiyani mukulimbana ndi ine?
Kodi ndakhala mtolo wolemera kwa inu?
-
-
Yobu 19:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Dziwani kuti ndi Mulungu amene wandisocheretsa,
Ndipo wandikola ndi ukonde wake wosakira nyama.
-