-
Miyambo 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Munthu amene amanyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,
Koma wosangalala ndi munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+
-