-
Maliro 4:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala.
Anthu sakuthanso kuwazindikira mʼmisewu.
Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo wouma.
-