Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+

      Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+

      Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+

  • Salimo 33:13-15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova amayangʼana padziko lapansi, kuchokera kumwamba.

      Iye amaona ana onse a anthu.+

      14 Kuchokera kumalo amene amakhala,

      Amayangʼanitsitsa anthu amene akukhala padziko lapansi.

      15 Iye ndi amene amaumba mitima ya anthu onse,

      Ndipo amafufuza ntchito zawo zonse.+

  • Yeremiya 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chifukwa maso anga akuona chilichonse chimene akuchita.*

      Anthuwo sanabisike kwa ine,

      Ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.

  • Yeremiya 23:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova.

      “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani