Salimo 143:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha chikondi chanu chokhulupirika, wonongani* adani anga.+Muwononge onse amene akundichitira nkhanza,+Chifukwa ine ndine mtumiki wanu.+
12 Chifukwa cha chikondi chanu chokhulupirika, wonongani* adani anga.+Muwononge onse amene akundichitira nkhanza,+Chifukwa ine ndine mtumiki wanu.+