Salimo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina la Yehova+ Wamʼmwambamwamba.+ Salimo 52:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani mpaka kalekale, chifukwa cha zimene mwachita.+Pamaso pa okhulupirika anu,Ndidzayembekezera dzina lanu,+ chifukwa ndi labwino.
17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina la Yehova+ Wamʼmwambamwamba.+
9 Ndidzakutamandani mpaka kalekale, chifukwa cha zimene mwachita.+Pamaso pa okhulupirika anu,Ndidzayembekezera dzina lanu,+ chifukwa ndi labwino.