2 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho akulu onse a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni ndipo Mfumu Davide inachita nawo pangano+ ku Heburoniko pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza Davide kuti akhale mfumu ya Isiraeli.+ Mlaliki 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikunena kuti: “Uzimvera malamulo a mfumu+ polemekeza lumbiro limene unachita kwa Mulungu.+
3 Choncho akulu onse a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni ndipo Mfumu Davide inachita nawo pangano+ ku Heburoniko pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza Davide kuti akhale mfumu ya Isiraeli.+