-
Miyambo 25:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Munthu wopereka umboni wabodza pa mlandu wa mnzake+
Ali ngati chibonga chakunkhondo, lupanga, komanso muvi wakuthwa.
-