-
Salimo 71:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Adani anga amandinenera zoipa,
Ndipo anthu amene akufuna kuchotsa moyo wanga, amandikonzera chiwembu,+
-
10 Adani anga amandinenera zoipa,
Ndipo anthu amene akufuna kuchotsa moyo wanga, amandikonzera chiwembu,+