-
Yeremiya 17:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Yehova wandiuza kuti: “Pita ukaime pageti la ana a anthu, pamene mafumu a Yuda amalowera ndi kutulukira komanso ukaime pamageti onse a mu Yerusalemu.+ 20 Ndipo ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mafumu a Yuda ndi anthu nonse amene mukukhala mu Yuda komanso inu nonse amene mukukhala mu Yerusalemu, amene mumalowera pamageti awa.
-