Salimo 37:23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova akasangalala ndi njira za munthu+Amamusonyeza zoyenera kuchita pa moyo wake.+ 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Chifukwa Yehova wamugwira dzanja kuti amuthandize.*+ 2 Akorinto 4:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
23 Yehova akasangalala ndi njira za munthu+Amamusonyeza zoyenera kuchita pa moyo wake.+ 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Chifukwa Yehova wamugwira dzanja kuti amuthandize.*+