-
Salimo 38:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthu amene akufunafuna moyo wanga anditchera misampha,
Amene akufuna kundivulaza akukambirana zoti andiwononge,+
Tsiku lonse iwo amapanga pulani yoti andinamize.
-