Salimo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa, amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo, koma mʼmitima yawo muli zinthu zoipa.+ Salimo 55:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu ake ndi osalala kuposa mafuta amumkaka,+Koma mumtima mwake amakonda nkhondo. Mawu ake ndi osalala kuposa mafuta,Koma ali ngati malupanga akuthwa.+
3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa, amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo, koma mʼmitima yawo muli zinthu zoipa.+
21 Mawu ake ndi osalala kuposa mafuta amumkaka,+Koma mumtima mwake amakonda nkhondo. Mawu ake ndi osalala kuposa mafuta,Koma ali ngati malupanga akuthwa.+