1 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide ankakhala mʼmalo ovuta kufikako kumapiri mʼchipululu cha Zifi.+ Sauli ankafunafuna Davide nthawi zonse,+ koma Yehova sanamʼpereke mʼmanja mwake.
14 Davide ankakhala mʼmalo ovuta kufikako kumapiri mʼchipululu cha Zifi.+ Sauli ankafunafuna Davide nthawi zonse,+ koma Yehova sanamʼpereke mʼmanja mwake.