-
Salimo 66:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Bwerani mudzamve, inu nonse amene mumaopa Mulungu,
Ndipo ine ndidzakuuzani zimene wandichitira.+
17 Ndinamuitana ndi pakamwa panga,
Ndipo ndinamutamanda ndi lilime langa.
-