-
Salimo 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma anthu onse amene amathawira kwa inu adzasangalala.+
Nthawi zonse adzafuula mosangalala.
Inu mudzawateteza kuti anthu oipa asawafikire,
Ndipo anthu okonda dzina lanu adzasangalala chifukwa cha inu.
-