Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 76:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu adzalowa mʼmapanga a muthanthweNdiponso mʼmayenje a munthaka,+Chifukwa cha kuopsa kwa mkwiyo wa YehovaNdiponso chifukwa cha ulemerero wake waukulu+Akaimirira kuti achititse dziko lapansi kunjenjemera ndi mantha. Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.
19 Anthu adzalowa mʼmapanga a muthanthweNdiponso mʼmayenje a munthaka,+Chifukwa cha kuopsa kwa mkwiyo wa YehovaNdiponso chifukwa cha ulemerero wake waukulu+Akaimirira kuti achititse dziko lapansi kunjenjemera ndi mantha.
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.