-
Numeri 6:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yehova asonyeze kuti akusangalala nanu+ ndipo akukomereni mtima.
-
-
Miyambo 16:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.
Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+
-