Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+