-
Salimo 22:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye.
Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+
-