-
Numeri 10:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Nthawi zonse Likasa likamanyamuka, Mose ankanena kuti: “Nyamukani, inu Yehova,+ adani anu abalalike. Ndipo amene amadana nanu athawe pamaso panu.”
-
-
Salimo 21:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.
Dzanja lanu lamanja lidzapeza anthu amene amadana nanu.
-