Yesaya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsiku limenelo mudzanena kuti: “Yamikani Yehova, itanani pa dzina lake,Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake.+ Lengezani kuti dzina lake ndi lokwezeka.+
4 Pa tsiku limenelo mudzanena kuti: “Yamikani Yehova, itanani pa dzina lake,Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake.+ Lengezani kuti dzina lake ndi lokwezeka.+