-
Oweruza 5:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+
Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,
Dziko linagwedezeka ndipo kumwamba kunagwetsa madzi,
Mitambo inagwetsa madzi.
-