-
Numeri 31:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Zinthuzo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa gulu lonse la anthuwo.+
-