-
Deuteronomo 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tinalanda mizinda yonse yakudera lokwererapo, mʼGiliyadi monse, mʼBasana monse, mpaka ku Saleka ndi ku Edirei,+ mizinda imene inali mu ufumu wa Ogi ku Basana.
-