-
Deuteronomo 7:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani.
-