-
Salimo 96:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu mabanja a mitundu ya anthu,
Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+
-