-
Salimo 144:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tambasulani manja anu kuchokera kumwamba.
Ndilanditseni ndi kundipulumutsa mʼmadzi amphamvu,
Ndilanditseni mʼmanja mwa anthu achilendo,+
-