-
Salimo 140:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Inu Yehova, nditetezeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+
Nditetezeni kwa anthu amene amachita zachiwawa.
Amene amakonza chiwembu kuti andivulaze.
-