-
Salimo 139:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Maso anu anandiona ngakhale pamene ndinali mluza.*
Ziwalo zanga zonse zinalembedwa mʼbuku lanu
Mʼbukumo munalembedwa za masiku amene zinapangidwa,
Zinalembedwa chiwalo chilichonse chisanapangidwe.
-