Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+ Salimo 89:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndi ndani kumwamba amene angafanane ndi Yehova?+ Ndi ndani pakati pa ana a Mulungu+ amene ndi wofanana ndi Yehova? Yeremiya 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ndi ndani amene sakuyenera kukuopani, inu Mfumu ya mitundu yonse?+ Inuyo ndinu woyenera kuopedwa.Chifukwa pakati pa anzeru onse a mʼmitundu ya anthu ndiponso pakati pa maufumu awo onse,Palibiretu aliyense wofanana ndi inu.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+
6 Ndi ndani kumwamba amene angafanane ndi Yehova?+ Ndi ndani pakati pa ana a Mulungu+ amene ndi wofanana ndi Yehova?
7 Kodi ndi ndani amene sakuyenera kukuopani, inu Mfumu ya mitundu yonse?+ Inuyo ndinu woyenera kuopedwa.Chifukwa pakati pa anzeru onse a mʼmitundu ya anthu ndiponso pakati pa maufumu awo onse,Palibiretu aliyense wofanana ndi inu.+