-
1 Mafumu 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno Yezebeli anamuuza kuti: “Kodi siinu amene mukulamulira Aisiraeli? Dzukani mudye ndipo musangalale. Ineyo ndikupatsani munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli.”+
-