-
Yobu 34:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kodi pali munthu wina wofanana ndi Yobu,
Amene amamwa mawu onyoza ngati madzi?
-
-
Yobu 34:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chifukwa wanena kuti, ‘Munthu sapindula chilichonse
Akamayesetsa kuchita zosangalatsa Mulungu.’+
-