Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Yehova wasankha Ziyoni.+Akufunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye akuti:+
2 Phiri la Ziyoni limene lili mʼdera lakutali lakumpoto,Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka komanso anthu padziko lonse lapansi akusangalala nalo,+Ndipo ndi mzinda wa Mfumu Yaikulu.+