2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 64:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nyumba yathu yoyera* ndiponso yaulemerero,*Imene makolo athu ankakutamandiranimo,Yawotchedwa ndi moto,+Ndipo zinthu zathu zonse zimene tinkaziona kuti ndi zamtengo wapatali zasanduka mabwinja
11 Nyumba yathu yoyera* ndiponso yaulemerero,*Imene makolo athu ankakutamandiranimo,Yawotchedwa ndi moto,+Ndipo zinthu zathu zonse zimene tinkaziona kuti ndi zamtengo wapatali zasanduka mabwinja