-
Salimo 13:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kodi ndidzapitiriza kuvutika ndi nkhawa,
Komanso tsiku lililonse ndidzakhala ndi chisoni mumtima mwanga mpaka liti?
Kodi mdani wanga adzapambana mpaka liti?+
-