-
Salimo 89:50, 51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Inu Yehova, kumbukirani mmene atumiki anu anyozedwera.
Kumbukirani mmene ndapiririra* kunyozedwa kochokera ku mitundu yonse ya anthu.
51 Inu Yehova, kumbukirani mmene adani anu alankhulira monyoza.
Mmene anyozera paliponse pamene mapazi a wodzozedwa wanu aponda.
-
-
Yesaya 52:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Tsopano kodi nditani pamenepa?” akutero Yehova.
“Chifukwa anthu anga anatengedwa kwaulere.
-