1 Samueli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova amasaukitsa ndiponso amalemeretsa,+Iye amatsitsa komanso amakweza.+ Danieli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+Amachotsa mafumu komanso kuika mafumu,+Amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+ Danieli 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Luka 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+Amachotsa mafumu komanso kuika mafumu,+Amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+