-
2 Mbiri 20:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Maufumu onse amʼdzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli, anakhala ndi mantha ochokera kwa Mulungu.+
-
-
Salimo 2:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Amene wakhala pampando wachifumu kumwamba adzaseka.
Yehova adzawanyogodola.
5 Pa nthawiyo, adzalankhula nawo atakwiya,
Ndipo adzawachititsa mantha ndi mkwiyo wake.
-