Salimo 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ine ndinapanikizika nʼkunena kuti: “Ndifa ndipo simudzandionanso.”+ Koma inu munamva kuchonderera kwanga kopempha thandizo pamene ndinafuulira kwa inu.+
22 Koma ine ndinapanikizika nʼkunena kuti: “Ndifa ndipo simudzandionanso.”+ Koma inu munamva kuchonderera kwanga kopempha thandizo pamene ndinafuulira kwa inu.+