-
Salimo 85:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kodi mutikwiyira mpaka kalekale?+
Kodi mudzapitiriza kusonyeza mkwiyo wanu ku mibadwomibadwo?
-
-
Yesaya 64:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Musatikwiyire kwambiri inu Yehova,+
Ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.
Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndi anthu anu.
-