Salimo 69:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo musabise nkhope yanu kwa mtumiki wanu.+ Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndili pamavuto aakulu.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+Ndipo chifundo chake sichitha.+
17 Ndipo musabise nkhope yanu kwa mtumiki wanu.+ Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndili pamavuto aakulu.+
22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+Ndipo chifundo chake sichitha.+