Yeremiya 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova wanena kuti: “Anthu onse oipa amene ndinayandikana nawo amene akukhudza cholowa chimene ndinapatsa anthu anga Aisiraeli kuti chikhale chawo,+ ndikuwazula mʼdziko lawo+ ndipo ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pawo.
14 Yehova wanena kuti: “Anthu onse oipa amene ndinayandikana nawo amene akukhudza cholowa chimene ndinapatsa anthu anga Aisiraeli kuti chikhale chawo,+ ndikuwazula mʼdziko lawo+ ndipo ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pawo.