Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 95:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa iye ndi Mulungu wathuNdipo ife ndi anthu amene iye akuweta,Nkhosa zimene akuzisamalira.*+ Lero anthu inu mukamvera mawu ake,+ Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani* kuti Yehova ndi Mulungu.+ Iye ndi amene anatipanga, ndipo ndife ake.+ Ndife anthu ake komanso nkhosa zimene akuweta.+
7 Chifukwa iye ndi Mulungu wathuNdipo ife ndi anthu amene iye akuweta,Nkhosa zimene akuzisamalira.*+ Lero anthu inu mukamvera mawu ake,+ Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani* kuti Yehova ndi Mulungu.+ Iye ndi amene anatipanga, ndipo ndife ake.+ Ndife anthu ake komanso nkhosa zimene akuweta.+
3 Dziwani* kuti Yehova ndi Mulungu.+ Iye ndi amene anatipanga, ndipo ndife ake.+ Ndife anthu ake komanso nkhosa zimene akuweta.+