Salimo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa, amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo, koma mʼmitima yawo muli zinthu zoipa.+
3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa, amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo, koma mʼmitima yawo muli zinthu zoipa.+