-
Oweruza 8:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Zeba ndi Zalimuna anati: “Nyamuka iweyo utiphe wekha. Munthu amaweruzidwa mogwirizana ndi mphamvu zake.” Ndiyeno Gidiyoni ananyamuka nʼkupha Zeba ndi Zalimuna,+ ndipo anatenga zokongoletsa zooneka ngati mwezi zimene zinali pamakosi a ngamila zawo.
-