-
Yesaya 17:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri.
Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.
Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiri
Ndiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.
-