Mlaliki 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa anthu ochita zoipa sanalangidwe mwamsanga,+ anthu atsimikiza mtima kuchita zoipa.+