-
Salimo 90:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Chifukwa ife tawonongedwa ndi mkwiyo wanu,+
Ndipo tikuchita mantha kwambiri ndi ukali wanu.
-
-
Salimo 102:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Izi zili choncho chifukwa cha mkwiyo ndi ukali wanu,
Popeza munandikweza mʼmwamba kuti munditaye.
-