-
Mlaliki 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndaona anthu oipa akuikidwa mʼmanda, amene ankalowa ndi kutuluka mʼmalo oyera, koma sanachedwe kuiwalika mumzinda umene ankachitiramo zinthu zoipa.+ Izinso nʼzachabechabe.
-